Yohane 4:11 - Buku Lopatulika11 Mkaziyo ananena ndi Iye, Ambuye, mulibe chotungira madzi, ndi chitsime chili chakuya; ndipo mwatenga kuti madzi amoyo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Mkaziyo ananena ndi Iye, Ambuye, mulibe chotungira madzi, ndi chitsime chili chakuya; ndipo mwatenga kuti madzi amoyo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Maiyo adati, “Bambo, mulibe nchotungira chomwe, ndipo chitsimechi nchozama. Nanga madzi opatsa moyowo muŵatenga kuti? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mayiyo anati, “Ambuye, Inu mulibe kanthu kotungira madzi ndipo chitsime ndi chakuya. Kodi madzi amoyowo mungawatenge kuti? Onani mutuwo |