Yohane 3:8 - Buku Lopatulika8 Mphepo iomba pomwe ifuna, ndipo ukumva mau ake, koma sudziwa kumene ichokera, ndi kumene imuka; chotero aliyense wobadwa mwa Mzimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mphepo iomba pomwe ifuna, ndipo ukumva mau ake, koma sudziwa kumene ichokera, ndi kumene imuka; chotero aliyense wobadwa mwa Mzimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mphepo imaombera komwe ikufuna, ndipo umamva kuwomba kwake, koma sudziŵa komwe yachokera kapena komwe ikupita. Nchimodzimodzi munthu aliyense amene abadwa mwa Mzimu Woyera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mphepo imawomba kulikonse kumene ikufuna. Ungathe kumva kuwomba kwake, koma sungathe kudziwa kumene ikuchokera kapena kumene ikupita. Nʼchimodzimodzi ndi amene abadwa ndi Mzimu Woyera.” Onani mutuwo |