Yohane 3:7 - Buku Lopatulika7 Usadabwe chifukwa ndinati kwa iwe, Uyenera kubadwa mwatsopano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Usadabwe chifukwa ndinati kwa iwe, Uyenera kubadwa mwatsopano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Usadabwe m'mene ndakuuza kuti muyenera kubadwanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwe usadabwe chifukwa ndakuwuza kuti, ‘Uyenera kubadwanso.’ Onani mutuwo |