Yohane 3:6 - Buku Lopatulika6 Chobadwa m'thupi chikhala thupi, ndipo chobadwa mwa Mzimu, chikhala mzimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chobadwa m'thupi chikhala thupi, ndipo chobadwa mwa Mzimu, chikhala mzimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Chobadwa mwa munthu ndi thupi chabe, koma chobadwa mwa Mzimu Woyera ndi mzimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Thupi limabereka thupi, koma Mzimu amabereka mzimu. Onani mutuwo |