Yohane 3:25 - Buku Lopatulika25 Pamenepo padauka kufunsana mwa ophunzira ake a Yohane ndi Myuda za mayeretsedwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pamenepo padauka kufunsana mwa ophunzira ake a Yohane ndi Myuda za mayeretsedwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ophunzira ena a Yohane adayamba kukangana ndi Myuda wina pa za mwambo wa kuyeretsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mkangano unabuka pakati pa ophunzira ena a Yohane ndi Ayuda ena pa zamwambo wodziyeretsa wa Ayuda. Onani mutuwo |