Yohane 3:22 - Buku Lopatulika22 Zitapita izi anadza Yesu ndi ophunzira ake kudziko la Yudeya; ndipo pamenepo anatsotsa nao pamodzi, nabatiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Zitapita izi anadza Yesu ndi ophunzira ake kudziko la Yudeya; ndipo pamenepo anatsotsa nao pamodzi, nabatiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pambuyo pake Yesu ndi ophunzira ake adapita ku dera la Yudeya. Adakhala nawo kumeneko kanthaŵi, ndipo ankabatiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Zitatha izi, Yesu ndi ophunzira ake anapita mʼmadera a ku midzi ya ku Yudeya, kumene Iye anakhala kanthawi akubatiza. Onani mutuwo |