Yohane 3:21 - Buku Lopatulika21 Koma wochita choonadi adza kukuunika, kuti ntchito zake zionekere kuti zinachitidwa mwa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma wochita choonadi adza kukuunika, kuti ntchito zake zionekere kuti zinachitidwa mwa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma wochita zokhulupirika amaonekera poyera, ndipo zochita zake zimadziŵika kuti wazichita momvera Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma aliyense wokhala mu choonadi amabwera ku kuwunika, kuti zionekere poyera zimene iye wachita zachitika kudzera mwa Mulungu.” Onani mutuwo |