Yohane 3:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo monga Mose anakweza njoka m'chipululu, chotero Mwana wa Munthu ayenera kukwezedwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo monga Mose anakweza njoka m'chipululu, chotero Mwana wa Munthu ayenera kukwezedwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 “Monga momwe Mose adaapachikira njoka pa mtengo m'chipululu muja, momwemonso Mwana wa Munthu ayenera kudzapachikidwa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsono monga Mose anapachika njoka mʼchipululu, moteronso Mwana wa Munthu ayenera kupachikidwa, Onani mutuwo |