Yohane 3:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo kulibe munthu anakwera Kumwamba, koma Iye wotsikayo kuchokera Kumwamba, ndiye Mwana wa Munthu, wokhala mu Mwambayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo kulibe munthu anakwera Kumwamba, koma Iye wotsikayo kuchokera Kumwamba, ndiye Mwana wa Munthu, wokhala m'Mwambayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Palibe munthu amene adakwera kupita Kumwamba, koma Mwana wa Munthu ndiye adatsika kuchokera Kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Palibe wina aliyense anapita kumwamba, koma yekhayo amene watsika kuchokera kumwamba, Mwana wa Munthu. Onani mutuwo |