Yohane 3:12 - Buku Lopatulika12 Ngati ndakuuzani za pansi pano, ndipo simukhulupirira, mudzakhulupirira bwanji, ngati ndikuuzani za Kumwamba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ngati ndakuuzani za pansi pano, ndipo simukhulupirira, mudzakhulupirira bwanji, ngati ndikuuzani za Kumwamba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ngati simukhulupirira pamene ndikukuuzani zapansipano, nanga mudzakhulupirira bwanji ndikadzakuuzani za Kumwamba? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine ndikuyankhula kwa iwe zinthu za dziko lapansi ndipo sukukhulupirira. Nanga kodi udzakhulupirira bwanji ngati nditayankhula zinthu zakumwamba? Onani mutuwo |