Yohane 21:21 - Buku Lopatulika21 Pamenepo Petro pakumuona, ananena kwa Yesu, Ambuye, koma nanga uyu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamenepo Petro pakumuona, ananena kwa Yesu, Ambuye, koma nanga uyu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pamene Petro adamuwona iyeyo, adafunsa Yesu kuti, “Ambuye, nanga uyu bwanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Petro atamuona iye, anafunsa kuti, “Ambuye, nanga uyu?” Onani mutuwo |