Yohane 21:20 - Buku Lopatulika20 Petro, m'mene anacheuka, anapenya wophunzira amene Yesu anamkonda alikutsata, amenenso anatsamira pachifuwa pake pamgonero, nati, Ambuye, ndani iye wakupereka Inu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Petro, m'mene anacheuka, anapenya wophunzira amene Yesu anamkonda alikutsata, amenenso anatsamira pachifuwa pake pamgonero, nati, Ambuye, ndani iye wakupereka Inu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Petro adacheuka, naona wophunzira uja amene Yesu ankamukonda kwambiri akuŵatsatira. Ndiye wophunzira yemwe uja amene adaatsamira pa chifukwa cha Yesu paphwando paja namufunsa kuti, “Ambuye, amene adzakuperekani kwa adani anu ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Petro anatembenuka ndi kuona kuti ophunzira amene Yesu amamukonda amawatsatira iwo. (Uyu ndi amene anatsamira pachifuwa cha Yesu pa chakudya chamadzulo ndipo iye anati, “Ambuye, kodi ndi ndani amene adzakuperekani Inu?” Onani mutuwo |