Yohane 21:13 - Buku Lopatulika13 Yesu anadza natenga mkate napatsa iwo, momwemonso nsomba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Yesu anadza natenga mkate napatsa iwo, momwemonso nsomba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yesu adadza natenga buledi uja nkuŵapatsa. Adateronso ndi nsomba zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yesu anabwera, natenga buledi ndikuwapatsa iwo, ndipo anachita chimodzimodzi ndi nsomba. Onani mutuwo |