Yohane 20:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo tsono analowanso wophunzira winayo, amene anayamba kufika kumanda, ndipo anaona, nakhulupirira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo tsono analowanso wophunzira winayo, amene anayamba kufika kumanda, ndipo anaona, nakhulupirira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamenepo wophunzira wina uja, amene adaayambira kufika ku manda, nayenso adaloŵa; ndipo ataona zimenezi, adakhulupirira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pomaliza wophunzira winayo, amene anafika ku manda moyambirira, analowanso mʼkati, iye anaona ndi kukhulupirira. Onani mutuwo |