Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 20:7 - Buku Lopatulika

7 ndi mlezo, umene unali pamutu pake, wosakhala pamodzi ndi nsalu zabafuta, koma wopindika padera pamalo pena.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 ndi mlezo, umene unali pamutu pake, wosakhala pamodzi ndi nsalu zabafuta, koma wopindika padera pamalo pena.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 ndiponso kansalu kamene kanali kumutu kwake. Kansaluko sikanali pamodzi ndi nsalu zina zija, koma padera pakokha, kali chipindire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 pamodzinso ndi nsalu imene anakulungira nayo mutu wa Yesu. Nsaluyi inali yopindidwa pa yokha yosiyanitsidwa ndi inayo.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:7
4 Mawu Ofanana  

Ndipo wina anadza, nanena, Mbuye, taonani, siyi mina yanu, ndaisunga m'kansalu;


Ndipo womwalirayo anatuluka womangidwa miyendo ndi manja ndi nsalu za kumanda; ndi nkhope yake inazingidwa ndi mlezo. Yesu ananena nao, Mmasuleni iye, ndipo mlekeni amuke.


Pamenepo anatenga mtembo wa Yesu, nauzenenga ndi nsalu zabafuta pamodzi ndi zonunkhira, monga mwa maikidwe a maliro a Ayuda.


Pamenepo anadzanso Simoni Petro alikumtsata iye, nalowa m'manda; ndipo anaona nsalu zabafuta zitakhala,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa