Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 20:6 - Buku Lopatulika

6 Pamenepo anadzanso Simoni Petro alikumtsata iye, nalowa m'manda; ndipo anaona nsalu zabafuta zitakhala,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Pamenepo anadzanso Simoni Petro alikumtsata iye, nalowa m'manda; ndipo anaona nsalu zabafuta zitakhala,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Simoni Petro atafika akumutsatira, adaloŵa m'mandamo. Adaona nsalu zija zili chikhalire,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Kenaka Simoni Petro, amene anali pambuyo pake, anafika ndi kulowa mʼmanda. Iye anaona nsaluzo zili pamenepo,

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:6
9 Mawu Ofanana  

Pamenepo mdzakazi wapakhomoyo ananena kwa Petro, Kodi suli iwenso wa ophunzira a munthu uyu? Iyeyu ananena, Sindine.


ndipo m'mene anawerama chosuzumira anaona nsalu zabafuta zitakhala, komatu sanalowemo.


ndi mlezo, umene unali pamutu pake, wosakhala pamodzi ndi nsalu zabafuta, koma wopindika padera pamalo pena.


Pamenepo wophunzira uja amene Yesu anamkonda ananena kwa Petro, Ndiye Ambuye. Simoni Petro pakumva kuti ndiye Ambuye, anadziveka malaya a pathupi, pakuti anali wamaliseche, nadziponya yekha m'nyanja.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa