Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 20:5 - Buku Lopatulika

5 ndipo m'mene anawerama chosuzumira anaona nsalu zabafuta zitakhala, komatu sanalowemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 ndipo m'mene anawerama chosuzumira anaona nsalu zabafuta zitakhala, komatu sanalowamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Adaŵerama naona nsalu zija zili chikhalire, koma iye sadaloŵemo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndipo mmene anawerama nasuzumira mʼkati mwa manda anaona nsalu zili potero koma sanalowemo.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:5
5 Mawu Ofanana  

Ndipo womwalirayo anatuluka womangidwa miyendo ndi manja ndi nsalu za kumanda; ndi nkhope yake inazingidwa ndi mlezo. Yesu ananena nao, Mmasuleni iye, ndipo mlekeni amuke.


Pamenepo anatenga mtembo wa Yesu, nauzenenga ndi nsalu zabafuta pamodzi ndi zonunkhira, monga mwa maikidwe a maliro a Ayuda.


Koma Maria analikuima kumanda kunja, alikulira. Ndipo m'mene alikulira anawerama chisuzumirire kumanda;


Koma anathamanga onse awiri pamodzi; ndipo wophunzira winayo anathamanga naposa Petro, nayamba kufika kumanda;


Pamenepo anadzanso Simoni Petro alikumtsata iye, nalowa m'manda; ndipo anaona nsalu zabafuta zitakhala,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa