Yohane 20:4 - Buku Lopatulika4 Koma anathamanga onse awiri pamodzi; ndipo wophunzira winayo anathamanga naposa Petro, nayamba kufika kumanda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma anathamanga onse awiri pamodzi; ndipo wophunzira winayo anathamanga naposa Petro, nayamba kufika kumanda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Onse aŵiri adathamanga pamodzi, koma wophunzira wina uja adathamanga kopambana Petro, nkuyambira ndiye kufika kumandako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Onse awiri anathamanga pamodzi koma wophunzira winayo anamupitirira Petro, nafika ku manda moyambirira. Onani mutuwo |