Yohane 20:3 - Buku Lopatulika3 Anatuluka tsono Petro ndi wophunzira winayo, nalinkupita kumanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Anatuluka tsono Petro ndi wophunzira winayo, nalinkupita kumanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pamenepo Petro ndi wophunzira wina uja adatuluka napita ku manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho Petro ndi wophunzira winayo ananyamuka kupita ku manda. Onani mutuwo |