Yohane 20:11 - Buku Lopatulika11 Koma Maria analikuima kumanda kunja, alikulira. Ndipo m'mene alikulira anawerama chisuzumirire kumanda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma Maria analikuima kumanda kunja, alikulira. Ndipo m'mene alikulira anawerama chisuzumirire kumanda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Maria adakhalabe chilili panja pafupi ndi manda, akulira. Akulira choncho, adaŵerama kusuzumira m'mandamo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 koma Mariya anayima kunja kwa manda akulira. Pamene akulira, anawerama ndi kusuzumira mʼmanda Onani mutuwo |