Yohane 20:12 - Buku Lopatulika12 ndipo anaona angelo awiri atavala zoyera, alikukhala mmodzi kumutu, ndi wina kumiyendo, kumene mtembo wa Yesu udagona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 ndipo anaona angelo awiri atavala zoyera, alikukhala mmodzi kumutu, ndi wina kumiyendo, kumene mtembo wa Yesu udagona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 naona angelo aŵiri ovala zovala zoyera. Angelowo adaakhala pansi, wina kumutu, wina kumapazi pamalo pamene padaagona mtembo wa Yesu paja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 ndipo anaona angelo awiri atavala zoyera, atakhala pamene panali mtembo wa Yesu, mmodzi kumutu ndi wina kumapazi. Onani mutuwo |