Yohane 20:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake ophunzirawo anachokanso, kunka kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake ophunzirawo anachokanso, kunka kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pambuyo pake ophunzirawo adabwerera kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kenaka ophunzira anabwerera ku nyumba zawo, Onani mutuwo |