Yohane 2:4 - Buku Lopatulika4 Yesu nanena naye, Mkazi, ndili ndi chiyani ndi inu? Nthawi yanga siinafike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Yesu nanena naye, Mkazi, ndili ndi chiyani ndi inu? Nthawi yanga siinafike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Yesu adayankha kuti, “Mai, kodi mukuti nditani? Nthaŵi yangatu siinafike.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yesu anayankha kuti, “Amayi, chifukwa chiyani mukundiwuza Ine? Nthawi yanga sinakwane.” Onani mutuwo |