Yohane 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo pakutha vinyo, amake wa Yesu ananena naye, Alibe vinyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo pakutha vinyo, amake wa Yesu ananena naye, Alibe vinyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pamene vinyo adatha, amai ake a Yesu adamuuza kuti, “Waŵathera vinyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Vinyo atatha, amayi a Yesu anati kwa Iye, “Wawathera vinyo.” Onani mutuwo |