Yohane 2:20 - Buku Lopatulika20 Pamenepo Ayuda anati, Zaka makumi anai ndi zisanu ndi chimodzi analimkumanga Kachisiyu, kodi inu mudzamuutsa masiku atatu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pamenepo Ayuda anati, Zaka makumi anai ndi zisanu ndi chimodzi analimkumanga Kachisiyu, kodi inu mudzamuutsa masiku atatu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Apo iwo adati, “Nyumba ya Mulunguyi idatenga zaka 46 kuti aimange, tsono Inu nkuimanga masiku atatu chabe?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ayuda anayankha kuti, “Zinatenga zaka makumi anayi kumanga Nyumbayi, kodi Inu mungayimange masiku atatu?” Onani mutuwo |