Yohane 2:21 - Buku Lopatulika21 Koma Iye analikunena za Kachisi wa thupi lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Iye analikunena za Kachisi wa thupi lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma Yesu ankanena za thupi lake mophiphiritsa, pamene adaatchula Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma Nyumba ya Mulungu imene amanena linali thupi lake. Onani mutuwo |