Yohane 2:17 - Buku Lopatulika17 Ophunzira ake anakumbukira kuti kunalembedwa, Changu cha pa nyumba yanu chandidya ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ophunzira ake anakumbukira kuti kunalembedwa, Changu cha pa nyumba yanu chandidya ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ophunzira ake adakumbukira Malembo aja akuti, “Changu chomwe ndimachitira nyumba yanu chidzandiphetsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ophunzira ake anakumbukira kuti zinalembedwa kuti, “Kudzipereka kwanga ku nyumba yanu kudzandiphetsa.” Onani mutuwo |