Yohane 19:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo pamene Pilato anamva mau awa, anaopa koposa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo pamene Pilato anamva mau awa, anaopa koposa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamene Pilato adamva mau ameneŵa, adachita mantha kwabasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pilato atamva zimenezi, anachita mantha kwambiri, Onani mutuwo |