Yohane 19:7 - Buku Lopatulika7 Ayuda anamyankha iye, Tili nacho chilamulo ife, ndipo monga mwa chilamulocho ayenera kufa, chifukwa anadziyesera Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ayuda anamyankha iye, Tili nacho chilamulo ife, ndipo monga mwa chilamulocho ayenera kufa, chifukwa anadziyesera Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Anthuwo adati, “Ife tili ndi lamulo, ndipo potsata lamulolo ayenera kufa, chifukwa ankati, ‘Ndine Mwana wa Mulungu.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ayuda anayimirira nati, “Ife tili ndi lamulo, ndipo molingana ndi lamulolo, Iyeyu ayenera kuphedwa chifukwa akudzitcha kuti ndi Mwana wa Mulungu.” Onani mutuwo |