Yohane 19:21 - Buku Lopatulika21 Pamenepo ansembe aakulu a Ayuda, ananena kwa Pilato, Musalembe, Mfumu ya Ayuda; koma kuti Iyeyu anati, Ndili mfumu ya Ayuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamenepo ansembe aakulu a Ayuda, ananena kwa Pilato, Musalembe, Mfumu ya Ayuda; koma kuti Iyeyu anati, Ndili mfumu ya Ayuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Akulu a ansembe a Ayuda adauza Pilato kuti, “Musalembe kuti, ‘Mfumu ya Ayuda’ ai, koma kuti, ‘Iyeyu ankati Ndine Mfumu ya Ayuda.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kenaka mkulu wa ansembe wa Ayuda anakadandaula kwa Pilato nati, “Musalembe kuti ‘Mfumu ya Ayuda,’ koma kuti munthuyu amadzitcha kuti ndi mfumu ya Ayuda.” Onani mutuwo |