Yohane 19:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo asilikali, m'mene analuka korona waminga anamveka pamutu pake, namfunda Iye malaya achibakuwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo asilikali, m'mene analuka korona waminga anamveka pamutu pake, namfunda Iye malaya achibakuwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono asilikali adaluka nsangamutu yaminga naiika pamutu pake. Adamuveka chovala chofiirira, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Asilikali analuka nkhata yaminga ndi kumuveka pamutu pake. Kenaka anamuveka mkanjo wapepo Onani mutuwo |