Yohane 19:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo tsono Pilato anatenga Yesu, namkwapula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo tsono Pilato anatenga Yesu, namkwapula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamenepo Pilato adalamula kuti atenge Yesu ndi kumkwapula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kenaka Pilato anatenga Yesu namukwapula mwankhanza. Onani mutuwo |