Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 18:40 - Buku Lopatulika

40 Pomwepo anafuulanso, nanena, Si uyu, koma Barabasi. Koma Barabasi anali wachifwamba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Pomwepo anafuulanso, nanena, Si uyu, koma Barabasi. Koma Barabasi anali wachifwamba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Pamenepo iwo adafuulanso kuti, “Ameneyu ai, koma Barabasi.” (Barabasiyo anali chigaŵenga.)

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Iwo anafuwula nati, “Ameneyu ayi! Mutipatse ife Baraba!” Barabayo anali wachifwamba.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:40
8 Mawu Ofanana  

Nthawi yomweyo Yesu anati kwa makamuwo a anthu, Kodi munatulukira kundigwira Ine ndi malupanga ndi mikunkhu, ngati wachifwamba? Tsiku ndi tsiku ndimakhala mu Kachisi kuphunzitsa, ndipo simunandigwire.


Ndipo pa nthawi yomweyo anali ndi wandende wodziwika, dzina lake Barabasi.


Pomwepo iye anamasulira iwo Barabasi, koma anakwapula Yesu, nampereka Iye kuti akampachike pamtanda.


Ndipo Pilato pofuna kuwakhazika mtima anthuwo, anawamasulira Barabasi, napereka Yesu, atamkwapula, akampachike pamtanda.


Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, womangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumpanduko.


Ndipo anawamasulira amene adaponyedwa m'ndende chifukwa cha mpanduko ndi kupha munthu, amene iwo anampempha; koma anapereka Yesu mwa chifuniro chao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa