Yohane 19:3 - Buku Lopatulika3 nadza kwa Iye, nanena, Tikuoneni, mfumu ya Ayuda! Nampanda khofu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 nadza kwa Iye, nanena, Tikuoneni, mfumu ya Ayuda! Nampanda khofu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 nadza kwa Iye nkumanena kuti, “Tikuwoneni, mfumu ya Ayuda!” Ndipo adayamba kumuwomba makofi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo ankapita kwa Iye mobwerezabwereza ndi kumanena kuti, “Moni mfumu ya Ayuda?” Ndipo amamumenya makofi. Onani mutuwo |