Yohane 19:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo pamenepo anampereka Iye kwa iwo kuti ampachike. Pamenepo anatenga Yesu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo pamenepo anampereka Iye kwa iwo kuti ampachike. Pamenepo anatenga Yesu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pamenepo Pilato adapereka Yesu kwa iwo kuti akampachike pa mtanda. Asilikali aja adamtenga Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pomaliza Pilato anamupereka kwa iwo kuti akapachikidwe. Choncho asilikali anamutenga Yesu. Onani mutuwo |