Yohane 18:7 - Buku Lopatulika7 Pamenepo anawafunsanso, Mufuna yani? Koma iwo anati, Yesu Mnazarayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pamenepo anawafunsanso, Mufuna yani? Koma iwo anati, Yesu Mnazarayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yesu adaŵafunsanso kuti, “Mukufuna yani kodi?” Iwo aja adati “Tikufuna Yesu wa ku Nazarete.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anawafunsanso kuti, “Kodi mukumufuna ndani?” Ndipo iwo anati, “Yesu wa ku Nazareti.” Onani mutuwo |