Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 18:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo m'mene anati kwa iwo, Ndine, anabwerera m'mbuyo, nagwa pansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo m'mene anati kwa iwo, Ndine, anabwerera m'mbuyo, nagwa pansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Pamene Yesu adaŵayankha kuti, “Ndine, ndilipo,” iwo adabwerera m'mbuyo nagwa pansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pamene Yesu anati, “Ndine,” iwo anabwerera mʼmbuyo ndi kugwa pansi.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:6
9 Mawu Ofanana  

Achite manyazi nabwerere m'mbuyo. Onse akudana naye Ziyoni.


Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa.


Achite manyazi nadodome iwo akulondola moyo wanga kuti auononge. Abwerere m'mbuyo, nachite manyazi iwo okondwera kundichitira choipa.


Anayankha Iye, Yesu Mnazarayo. Yesu ananena nao, Ndine. Koma Yudasi yemwe, wompereka Iye, anaima nao pamodzi.


Pamenepo anawafunsanso, Mufuna yani? Koma iwo anati, Yesu Mnazarayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa