Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 18:16 - Buku Lopatulika

16 koma Petro anaima kukhomo kunja. Chifukwa chake wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anatuluka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 koma Petro anaima kukhomo kunja. Chifukwa chake wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anatuluka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Koma Petro adaima pa khomo kunja. Wophunzira wina uja, amene anali wodziŵikayo, adatuluka nakalankhula ndi mtsikana wolonda pa khomo, nkumuloŵetsa Petroyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 koma Petro anadikira kunja pa khomo. Ophunzira winayo amene amadziwika kwa mkulu wa ansembe, anatuluka ndi kuyankhula ndi mtsikana amene anali mlonda wa pa khomo ndi kumulowetsa Petro.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:16
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Petro adakhala pabwalo: ndipo mdzakazi anadza kwa iye, nanena, Iwenso unali ndi Yesu wa ku Galileya.


Ndipo pa chikondwerero kazembe adazolowera kumasulira anthu mmodzi wandende, amene iwo anafuna.


Ndipo ankawamasulira pachikondwerero wandende mmodzi, amene iwo anampempha.


Koma iwo onse pamodzi anafuula, nati, Chotsani munthu uyu, mutimasulire Barabasi;


Ndipo m'mene anagogoda pa chitseko cha pakhomo, anadza kudzavomera mdzakazi, dzina lake Roda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa