Yohane 18:15 - Buku Lopatulika15 Koma Simoni Petro ndi wophunzira wina anatsata Yesu. Koma wophunzira ameneyo anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, nalowa pamodzi ndi Yesu, m'bwalo la mkulu wa ansembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma Simoni Petro ndi wophunzira wina anatsata Yesu. Koma wophunzira ameneyo anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, nalowa pamodzi ndi Yesu, m'bwalo la mkulu wa ansembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Simoni Petro ndi wophunzira wina adatsatira Yesu. Wophunzira winayo anali wodziŵika kwa mkulu wa ansembe onse. Tsono iye adaloŵa pamodzi ndi Yesu m'bwalo la nyumba ya mkulu wa ansembeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Simoni Petro ndi ophunzira wina ankamutsatira Yesu chifukwa ophunzira uyu amadziwika kwa mkulu wa ansembe. Iye analowa ndi Yesu mʼbwalo la mkulu wa ansembe Onani mutuwo |