Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 18:14 - Buku Lopatulika

14 Koma Kayafa anali uja wakulangiza Ayuda, kuti kuyenera munthu mmodzi afere anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Koma Kayafa anali uja wakulangiza Ayuda, kuti kuyenera munthu mmodzi afere anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Kayafayo ndi yemwe uja amene adaalangiza anzake kuti nkwabwino koposa kuti munthu mmodzi afe m'malo mwa anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Kayafa anali amene analangiza Ayuda kuti kukanakhala kwabwino ngati munthu mmodzi akanafera anthu.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:14
4 Mawu Ofanana  

Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa;


Ndipo popeza dooko silinakome kugonapo nyengo yachisanu, unyinji unachita uphungu ndi kuti amasule nachokepo, ngati kapena nkutheka afikire ku Fenikisi, ndi kugonako, ndilo dooko la ku Krete, loloza kumpoto ndi kumwera.


Ndipo itapita nthawi yambiri, ndipo unayambokhala woopsa ulendowo, popezanso nyengo ya kusala chakudya idapita kale, Paulo anawachenjeza,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa