Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 18:13 - Buku Lopatulika

13 nayamba kupita naye kwa Anasi; pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chomwecho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 nayamba kupita naye kwa Anasi; pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chomwecho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Poyamba adapita naye kwa Anasi, chifukwa anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe onse chaka chimenecho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Poyamba anapita naye kwa Anasi amene anali mkamwini wa Kayafa, mkulu wa ansembe chaka chimenecho.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 18:13
9 Mawu Ofanana  

Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa;


Ndipo iwo akugwira Yesu ananka naye kwa Kayafa, mkulu wa ansembe, kumene adasonkhana alembi ndi akulu omwe.


pa ukulu wansembe wao wa Anasi ndi Kayafa, panadza mau a Mulungu kwa Yohane mwana wa Zekariya m'chipululu.


Koma wina mmodzi wa mwa iwo, Kayafa, wokhala mkulu wa ansembe chaka chomwecho anati kwa iwo, Simudziwa kanthu konse inu,


Koma ichi sananene kwa iye yekha; koma pokhala mkulu wa ansembe chaka chomwecho ananenera kuti Yesu adzafera mtunduwo;


Koma Anasi adamtumiza Iye womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe.


Pamenepo anamtenga Yesu kuchokera kwa Kayafa kupita ku Pretorio; koma munali mamawa; ndipo iwo sanalowe ku Pretorio, kuti angadetsedwe, koma kuti akadye Paska.


Yesu anamyankha iye, Simukadakhala nao ulamuliro uliwonse pa Ine, ngati sukadapatsidwa kwa inu kuchokera Kumwamba; chifukwa cha ichi iye wondipereka Ine kwa inu ali nalo tchimo loposa.


ndi Anasi mkulu wa ansembe, ndi Kayafa, ndi Yohane, ndi Aleksandro, ndi onse amene anali a fuko la mkulu wa ansembe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa