Yohane 18:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo khamulo ndi kapitao wamkulu, ndi anyamata a Ayuda anagwira Yesu nammanga Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo khamulo ndi kapitao wamkulu, ndi anyamata a Ayuda anagwira Yesu nammanga Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Gulu la asilikali achiroma lija, pamodzi ndi mtsogoleri wao, ndiponso asilikali achiyuda, adagwira Yesu nammanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka gulu la asilikali ndi olamulira wawo ndi akuluakulu a Ayuda anamugwira Yesu. Iwo anamumanga. Onani mutuwo |