Yohane 17:9 - Buku Lopatulika9 Ine ndiwapempherera iwo; sindipempherera dziko lapansi, koma iwo amene mwandipatsa Ine, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ine ndiwapempherera iwo; sindipempherera dziko lapansi, koma iwo amene mwandipatsa Ine, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Ine ndikuŵapempherera. Sindikupempherera anthu ena onse, koma ndikupempherera iwoŵa amene mudandipatsa, chifukwa ndi anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ine ndikuwapempherera. Ine sindikupempherera dziko lapansi, koma anthu amene Inu mwandipatsa, pakuti ndi anu. Onani mutuwo |