Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 16:12 - Buku Lopatulika

12 Ndili nazo zambirinso zakunena kwa inu, koma simungathe kuzisenza tsopano lino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndili nazo zambirinso zakunena kwa inu, koma simungathe kuzisenza tsopano lino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Ndili nawo mau ena ambiri oti ndikuuzeni, koma simungathe kuŵamvetsa tsopano ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Ine ndili ndi zambiri zoti ndiyankhule nanu, koma simungathe kuzilandira tsopano.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 16:12
8 Mawu Ofanana  

Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, monga anakhoza kumva;


Sindidzalankhulanso zambiri ndi inu, pakuti mkulu wa dziko lapansi adza; ndipo alibe kanthu mwa Ine;


Sinditchanso inu akapolo; chifukwa kapolo sadziwa chimene mbuye wake achita; koma ndatcha inu abwenzi; chifukwa zonse zimene ndazimva kwa Atate wanga ndakudziwitsani.


za chiweruzo, chifukwa mkulu wa dziko ili lapansi waweruzidwa.


Koma atadza Iyeyo, Mzimu wa choonadi, adzatsogolera inu m'choonadi chonse; pakuti sadzalankhula za Iye mwini; koma zinthu zilizonse adzazimva, adzazilankhula; ndipo zinthu zilinkudza adzakulalikirani.


kwa iwonso anadzionetsera yekha wamoyo ndi zitsimikizo zambiri, zitatha zowawa zake, naonekera kwa iwo masiku makumi anai, ndi kunena zinthu za Ufumu wa Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa