Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 15:9 - Buku Lopatulika

9 Monga momwe Atate wandikonda Ine, Inenso ndakonda inu; khalani m'chikondi changa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Monga momwe Atate wandikonda Ine, Inenso ndakonda inu; khalani m'chikondi changa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 “Monga momwe Atate andikondera, Inenso ndakukondani. Muzikhala m'chikondi changachi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 “Monga momwe Atate amandikondera Ine, Inenso ndakukondani. Tsopano khalani mʼchikondi changa.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 15:9
9 Mawu Ofanana  

Izi ndalankhula ndi inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chidzale.


Palibe munthu ali nacho chikondi choposa ichi, chakuti munthu ataya moyo wake chifukwa cha abwenzi ake.


ndipo ndinazindikiritsa iwo dzina lanu, ndipo ndidzalizindikiritsa; kuti chikondi chimene munandikonda nacho chikhale mwa iwo, ndi Ine mwa iwo.


Atate akonda Mwana, nampatsa zinthu zonse m'dzanja lake.


mukakhozetu kuzindikira pamodzi ndi oyera mtima onse, kupingasa, ndi utali, ndi kukwera,


Ndipo tsopano, tiana, khalani mwa Iye; kuti akaonekere Iye tikakhale nako kulimbika mtima, osachita manyazi kwa Iye pa kudza kwake.


Koma inu, okondedwa, podzimangirira nokha pa chikhulupiriro chanu choyeretsetsa, ndi kupemphera mu Mzimu Woyera,


ndi kwa Yesu Khristu, mboni yokhulupirikayo, wobadwa woyamba wa akufa, ndi mkulu wa mafumu a dziko lapansi. Kwa Iye amene atikonda ife, natimasula kumachimo athu ndi mwazi wake;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa