Yohane 15:11 - Buku Lopatulika11 Izi ndalankhula ndi inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chidzale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Izi ndalankhula ndi inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chidzale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Ndakuuzani zimenezi kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, kuti chimwemwe chanu chikhale chathunthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ine ndakuwuzani izi kuti chimwemwe changa chikhale mwa Inu, kuti chimwemwe chanu chikhale chokwanira. Onani mutuwo |