Yohane 13:8 - Buku Lopatulika8 Petro ananena ndi Iye, Simudzasambitsa mapazi anga kunthawi yonse. Yesu anamyankha iye, Ngati sindikusambitsa iwe ulibe cholandira pamodzi ndi Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Petro ananena ndi Iye, Simudzasambitsa mapazi anga kunthawi yonse. Yesu anamyankha iye, Ngati sindikusambitsa iwe ulibe cholandira pamodzi ndi Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Petro adati, “Simudzandisambitsa konse mapazi.” Yesu adamuyankha kuti, “Ngati sindikusambitsa, ndiye kuti chako palibe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Petro anati, “Ayi, Inu simudzandisambitsa konse mapazi anga.” Yesu anayankha kuti, “Ngati Ine sindisambitsa mapazi ako, ulibe gawo mwa Ine.” Onani mutuwo |