Yohane 13:7 - Buku Lopatulika7 Yesu anayankha nati kwa iye, Chimene ndichita Ine suchidziwa tsopano; koma udzadziwa m'tsogolo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Yesu anayankha nati kwa iye, Chimene ndichita Ine suchidziwa tsopano; koma udzadziwa m'tsogolo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yesu adamuyankha kuti, “Zimene ndikuchitazi, sukuzidziŵa tsopano, koma udzazidziŵa m'tsogolo muno.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yesu anayankha kuti, “Iwe sukuzindikira tsopano chimene ndikuchita, koma udzazindikira mʼtsogolo.” Onani mutuwo |