Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 13:6 - Buku Lopatulika

6 Anadza pomwepo kwa Simoni Petro. Iyeyu ananena ndi Iye, Ambuye, kodi Inu mundisambitsa ine mapazi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Anadza pomwepo kwa Simoni Petro. Iyeyu ananena ndi Iye, Ambuye, kodi Inu mundisambitsa ine mapazi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Pamene adafika pa Simoni Petro, iyeyo adati, “Ambuye, Inuyo nkundisambitsa ine mapazi?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Atafika pa Petro, Petroyo anati kwa Iye, “Ambuye, kodi mudzandisambitsa mapazi anga?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 13:6
5 Mawu Ofanana  

Koma Simoni Petro, pamene anaona, anagwa pansi pa mawondo ake a Yesu, nanena, Muchoke kwa ine, Ambuye, chifukwa ndine munthu wochimwa.


ndiye wakudza pambuyo panga, amene sindiyenera kummasulira chingwe cha nsapato yake.


Pomwepo anathira madzi m'beseni, nayamba kusambitsa mapazi a ophunzira ake, ndi kuwapukuta ndi chopukutira, chimene anadzimanga nacho.


Yesu anayankha nati kwa iye, Chimene ndichita Ine suchidziwa tsopano; koma udzadziwa m'tsogolo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa