Yohane 13:9 - Buku Lopatulika9 Simoni Petro ananena ndi Iye, Ambuye, si mapazi anga okha, komanso manja ndi mutu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Simoni Petro ananena ndi Iye, Ambuye, si mapazi anga okha, komanso manja ndi mutu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Simoni Petro adati, “Ambuye, ngati ndi choncho, mutsuke osati mapazi anga okha, komanso manja anga ndi mutu womwe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Simoni Petro anayankha kuti, “Ambuye, osati mapazi okha komanso manja anga ndi mutu wanga womwe!” Onani mutuwo |